Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 48:23-25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

23. ndi pa Kiriataimu, ndi pa Beti-Gamuli, ndi pa Beti-Meoni;

24. ndi pa Kerioti, ndi pa Bozira, ndi pa midzi yonse ya dziko la Moabu, yakutari kapena yakufupi.

25. Nyanga ya Moabu yaduka, ndipo watyoka mkono wace, ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 48