Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 47:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova atero: Taonani, madzi adzakwera kuturuka kumpoto, nadzakhala mtsinje wosefuka, nadzasefukira padziko ndi pa zonse ziri m'mwemo, pamudzi ndi pa onse okhalamo; ndipo amuna adzalira, ndi onse okhala m'dziko adzakuwa.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 47

Onani Yeremiya 47:2 nkhani