Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 46:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli, ati: Taonani, ndidzalanga Amoni wa No, ndi Farao, ndi Aigupto, pamodzi ndi milungu yace, ndi mafumu ace; ngakhale Farao, ndi iwo akumkhulupirira iye;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 46

Onani Yeremiya 46:25 nkhani