Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 46:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndiponso olipidwa ace ali pakati pace onga ngati ana a ng'ombe a m'khola; pakuti iwonso abwerera, athawa pamodzi, sanaime; pakuti tsiku la tsoka lao linawafikira, ndi nthawi ya kuweruzidwa kwao.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 46

Onani Yeremiya 46:21 nkhani