Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 44:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli, Inu ndi akazi anu mwanena ndi m'kamwa mwanu, ndi kukwaniritsa ndi manja anu kuti, Tidzacita ndithu zowinda zathu taziwindira, kufukizira mfumu yaikazi ya kumwamba, ndi kumthirira iye nsembe zothira; khazikitsanitu zowinda zanu, citani zowinda zanu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 44

Onani Yeremiya 44:25 nkhani