Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 44:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli: Mwaona coipa conse cimene ndatengera pa Yerusalemu, ndi pa midzi yonse ya Yuda; ndipo, taonani, lero lomwe iri bwinja, palibe munthu wokhalamo;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 44

Onani Yeremiya 44:2 nkhani