Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 44:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma tidzacita ndithu mau onse anaturuka m'kamwa mwathu, kufukizira mfumu yaikazi ya kumwamba, ndi kumthirira iye nsembe zothira, monga momwe tikacitira ife, ndi atate athu, ndi mafumu athu ndi akuru athu, m'midzi ya Yuda, ndi m'miseu ya Yerusalemu, pakuti pamenepo tinali ndi cakudya cokwanira, tinakhala bwino, sitinaona coipa.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 44

Onani Yeremiya 44:17 nkhani