Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 43:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi amuna, ndi akazi, ndi ana, ndi ana akazi a mfumu, ndi anthu onse amene Nebuzaradani kapitao Wa alonda anasiya ndi Gedaliya mwana wace wa Ahikamu, mwana wace wa Safani, ndi Yeremiya mneneri, ndi Baruki mwana wace wa Neriya;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 43

Onani Yeremiya 43:6 nkhani