Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 43:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndidzayatsa moto m'nyumba za milungu ya Aigupto; ndipo adzazitentha, nadzaitenga ndende; ndipo adzadzipfunda ndi dziko la Aigupto, monga mbusa abvala cobvala cace; nadzaturuka m'menemo ndi mtendere.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 43

Onani Yeremiya 43:12 nkhani