Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 43:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi kuti kwa iwo, Atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli: Taonani Ine ndidzatuma ndidzatenga Nebukadirezara mfumu ya ku Babulo, mtumiki wanga, ndi kuika mpando wace wacifumu pa miyalayi ndaiyala; ndipo iye adzaibvundikira ndi hema wacifumu wace.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 43

Onani Yeremiya 43:10 nkhani