Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 4:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo padzakhala tsiku lomwelo, ati Yehova, kuti mtima wa mfumu udzatayika, ndi mitima ya akuru; ndipo ansembe adzazizwa, ndi aneneri adzadabwa.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 4

Onani Yeremiya 4:9 nkhani