Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 4:21-23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

21. Kufikira liti ndidzaona mbendera, ndi kumva kulira kwa lipenga?

22. Pakuti anthu anga apusa, sandidziwa Ine; ali ana opulukira sazindikira; ali ocenjera kucita coipa koma kucita cabwino sakudziwa.

23. Ndinaona dziko lapansi, ndi rpo taona, linali lopasuka lopanda kanthu; ndipo ndinaona kumwamba, kunalibe kuunika.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 4