Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 39:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma nkhondo ya Akasidi inawalondola, nimpeza Zedekiya m'zidikha za Yeriko; ndipo atamgwira, anamtengera kwa Nebukadirezara mfumu ya ku Babulo ku Ribila m'dziko la Hamati, ndipo iye ananena naye mlandu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 39

Onani Yeremiya 39:5 nkhani