Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 36:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu anatuma Yehudi atenge mpukutuwo; ndipo anautenga kuturuka nao m'cipinda ca Elisama mlembi, Ndipo Yehudi anauwerenga m'makutu a mfumu, ndi m'makutu a akuru onse amene anaima pambali pa mfumu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 36

Onani Yeremiya 36:21 nkhani