Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 36:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace akuru onse anatuma Yehudi mwana wa Nataniya, mwana wa Salamiya, mwana wa Kusa, kwa Baruki, kukanena, Tenga m'dzanja lako mpukutu wauwerenga m'makutu a anthu, nudze kuno. Ndipo Baruki mwana wa Neriya anatenga mpukutuwo m'dzanja lace, nadza kwa iwo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 36

Onani Yeremiya 36:14 nkhani