Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 35:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ife tamva mau a Yonadabu mwana wa Rekabu kholo lathu m'zonse zimene anatiuza ife, zakuti tisamwe vinyo masiku athu onse, ife, akazi athu, ana athu amuna ndi akazi;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 35

Onani Yeremiya 35:8 nkhani