Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 35:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma anati, Sitidzamwa vinyo; pakuti Yonadabu mwana wa Rekabu kholo lathu anatiuza ife, kuti, Musadzamwe vinyo, kapena inu, kapena ana anu, kumuyaya;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 35

Onani Yeremiya 35:6 nkhani