Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 34:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace Yehova atero: Simunandimvera Ine, kuti mulalikire ufulu, munthu yense kwa mbale wace, ndi munthu yense kwa mnzace; taonani, ndilalikira kwa inu ufulu, ati Yehova, wa kulupanga, kucaola, ndi kunjala; ndipo ndidzakuperekani mukhale oopsetsa m'maufumu onse a dziko lapansi.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 34

Onani Yeremiya 34:17 nkhani