Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 32:44 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anthu adzagula minda ndi ndalama, adzalembera akalata ogulira, adzawasindikiza, adzaitana mboni, m'dziko la Benjamini, ndi m'malo ozungulira Yerusalemu, ndi m'midzi ya Yuda, ndi m'midzi ya kumtunda, ndi m'midzi ya kucidikha, ndi m'midzi ya ku Mwera; pakuti ndidzabweza undende wao, ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 32

Onani Yeremiya 32:44 nkhani