Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 32:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo Zedekiya mfumu ya Yuda sadzapulumuka m'dzanja la Akasidi, koma adzaperekedwadi m'dzanja la mfumu ya Babulo, ndipo adzanena ndi iye pakamwa ndi pakamwa, ndipo adzaonana maso ndi maso;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 32

Onani Yeremiya 32:4 nkhani