Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 32:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anamanga misanje ya Baala, iri m'cigwaca mwana wace wa Hinomu, kuti apitirize kumoto ana ao amuna ndi akazi cifukwa ca Moleki; cimene sindinauza, cimene sicinalowa m'mtima mwanga, kuti acite conyansa ici, cocimwitsa Yuda.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 32

Onani Yeremiya 32:35 nkhani