Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 32:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

cifukwa ca zoipa zonse za ana a Israyeli ndi za ana a Yuda, zimene anandiputa nazo Ine, iwowo, mafumu ao, akulu ao, ansembe ao, aneneri ao, ndi anthu a Yuda, ndi okhala m'Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 32

Onani Yeremiya 32:32 nkhani