Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 32:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo ndinapereka kalata wogulirayo kwa Baruki mwana wa Neriya, mwana wa Maseya, pamaso pa Hanameli mwana wa mbale wa atate wanga, ndi pamaso pa mboni zimene zinalemba pa kalata wogulirayo, pamaso pa Ayuda onse okhala m'bwalo la kaidi.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 32

Onani Yeremiya 32:12 nkhani