Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 31:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, ndidzatenga iwo ku dziko la kumpoto, ndidzasonkhanitsa iwo ku malekezero a dziko lapansi, pamodzi ndi osaona ndi opunduka mwendo, mkazi amene ali ndi pakati ndi mkazi alinkubala pamodzi; khamu lalikuru lidzabwera kuno.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 31

Onani Yeremiya 31:8 nkhani