Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 31:40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo cigwa conse ca mitembo, ndi ca phulusa, ndi minda yonse: kufikira ku mtsinje wa Kidroni, kufikira kungondya kwa cipata ca akavalo kuloza kum'mawa, ponsepo padzapatulikira Yehova; sipadzazulidwa, sipadzagwetsedwa konse ku nthawi zamuyaya.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 31

Onani Yeremiya 31:40 nkhani