Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 31:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo padzakhala kuti, monga ndayang'anira iwo kuzula ndi kupasula ndi kugwetsa, ndi kuononga ndi kusautsa; momwemo ndidzayang'anira iwo kumangitsa mudzi ndi kubzyala, ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 31

Onani Yeremiya 31:28 nkhani