Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 31:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kumva ndamva Efraimu alinkulirira kotero, Mwandilanga ine, ndipo ndalangidwa, monga mwana wa ng'ombe wosazolowera gori; munditembenuze ine, ndipo ine ndidzatembenuka; pakuti inu ndinu Yehova Mulungu wanga.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 31

Onani Yeremiya 31:18 nkhani