Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 31:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo adzadza nadzayimba pa msanje wa Ziyoni, nadzasonkhanira, ku zokoma za Yehova, kutirigu, ndi kuvinyo, ndi mafuta, ndi kwa ana a zoweta zazing'ono ndi zazikuru; ndipo moyo wao udzakhala ngati munda wamicera; ndipo, sadzakhalanso konse ndi cisoni.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 31

Onani Yeremiya 31:12 nkhani