Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 31:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tamvani mau a Yehova, amitundu inu, lalikirani m'zisumbu zakutari; ndi kuti, Iye amene anabalalitsa Israyeli adzasonkhanitsa, nadzamsunga, monga mbusa acita ndi zoweta zace.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 31

Onani Yeremiya 31:10 nkhani