Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 30:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti, taona, masiku adzadza, ati Yehova, amene ndidzabwezanso undende wa anthu anga Aisrayeli ndi Ayuda, ati Yehova; ndipo ndidzawabwezera ku dziko limene ndinapatsa makolo ao. Ndipo adzakhala nalo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 30

Onani Yeremiya 30:3 nkhani