Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 30:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo padzaturuka pa izo mayamikiro ndi mau a iwo okondwerera; ndipo ndidzacurukitsa iwo, sadzakhala owerengeka; ndidzawacitiranso ulemu, sadzacepa.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 30

Onani Yeremiya 30:19 nkhani