Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 30:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace iwo akulusira iwe adzalusidwanso; ndi adani ako onse, adzanka kuundende onsewo; ndipo iwo adzakufunkha iwe adzakhala cofunkha, ndipo onse akulanda iwe ndidzapereka kuti zilandidwe zao.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 30

Onani Yeremiya 30:16 nkhani