Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 30:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo usaope, iwe Yakobo mtumiki wanga, ati Yehova; usaope, iwe Israyeli; pakuti, taona, ndidzakupulumutsa iwe kutari, ndi mbeu zako ku dziko la undende wao; ndipo Yakobo adzabwera, nadzakhala ndi mtendere, ndipo adzakhala cete, palibe amene adzamuopsya.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 30

Onani Yeremiya 30:10 nkhani