Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 3:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinaona, kuti, ndingakhale ndikamcotsa Israyeli wobwerera m'mbuyo, ndi kumpatsa kalata wacilekaniro cifukwa ca kucita cigololo iye, mphwace Yuda wonyenga sanaope, koma iye yemwe ananka nacita dama.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 3

Onani Yeremiya 3:8 nkhani