Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 3:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tigone m'manyazi athu, kunyala kwathu kutipfunde ife; pakuti tamcimwira Yehova Mulungu wathu, ife ndi makolo athu, kuyambira ubwana wathu kufikira lero lomwe; ndipo sitidamvera mau a Yehova Mulunguwathu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 3

Onani Yeremiya 3:25 nkhani