Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 3:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Ine ndinati, Ndidzakuika iwe bwanji mwa ana, ndi kupatsa iwe dziko lokondweretsa, colowa cabwino ca makamu a mitundu ya anthu? ndipo ndinati mudzandicha Ine, Atate wanga; osatembenuka kuleka kunditsata Ine.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 3

Onani Yeremiya 3:19 nkhani