Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 29:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzapezedwa ndi inu, ati Yehova, ndidzabwezanso undende wanu, ndipo ndidzasonkhanitsa inu kwa mitundu yonse, ndi kumalo konse kumene ndinakupitikitsirani inu, ati Yehova; ndipo ndidzakubwezeraninso kumalo kumene ndinakutengani inu andende.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 29

Onani Yeremiya 29:14 nkhani