Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 29:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Amenewa ndi mau a kalata uja anatumiza Yeremiya mneneri kucokera ku Yerusalemu kunka kwa akuru otsala a m'nsinga, ndi kwa ansembe, ndi kwa aneneri, ndi kwa anthu onse, amene Nebukadnezara anawatenga ndende ku Yerusalemu kunka ku Babulo;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 29

Onani Yeremiya 29:1 nkhani