Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 28:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo ndidzabwezeranso kumalo kuno Yekoniya mwana wace wa Yehoyakimu, mfumu ya Yuda, ndi am'nsinga onse a Yuda, amene ananka ku Babulo, ati Yehova: pakuti ndidzatyola gori la mfumu ya ku Babulo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 28

Onani Yeremiya 28:4 nkhani