Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 28:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Hananiya ananena pamaso pa anthu onse, kuti, Yehova atero: Comweco ndidzatyola gori la Nebukadinezara mfumu ya Babulo zisanapite zaka ziwiri zamphumphu kulicotsa pa khosi la amitundu onse. Ndipo Yeremiya mneneri anacoka.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 28

Onani Yeremiya 28:11 nkhani