Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 27:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo padzakhala, kuti mtundu ndi ufumu umene sudzamtumikira Nebukadinezara yemweyo mfumu ya ku Babulo, mtundu umenewo Ine ndidzalanga, ati Yehova, ndi lupanga, ndi njala, ndi caola, mpaka nditatha onse ndi dzanja lace.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 27

Onani Yeremiya 27:8 nkhani