Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 27:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Poyamba kukhala mfumu Yehoyakimu mwana wace wa Yosiya, mfumu ya Yuda, mau awa anadza kwa Yeremiya kucokera kwa Yehova, kuti,

2. Yehova atero kwa ine: Udzipangire zomangira ndi magori, nuziike pakhosi pako;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 27