Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 26:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo pamene Yehoyakimu mfumu, ndi amphamvu ace onse, ndi akuru onse, anamva mau ace, mfumu inafuna kumupha iye; koma pamene Uriya anamva, anaopa, nathawa, nanka ku Aigupto;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 26

Onani Yeremiya 26:21 nkhani