Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 26:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mudziwe ndithu kuti, ngati mudzandipha ine, mudzadzitengera nokha mwazi wosacimwa, ndi pa mudzi uwu, ndi pa okhalamo ace; pakuti mwa ntheradi Yehova wandituma kwa inu kuti ndinene mau onse awa m'makutu anu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 26

Onani Yeremiya 26:15 nkhani