Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 26:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace tsopano konzani njira zanu ndi macitidwe anu, ndi kumvera mau a Yehova Mulungu wanu; ndipo Yehova adzaleka coipa cimene ananenera inu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 26

Onani Yeremiya 26:13 nkhani