Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 26:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ansembe ndi aneneri ananena kwa akuru ndi kwa anthu onse, kuti, Munthu uyu ayenera kufa; pakuti wanenera mudzi uwu monga mwamva ndi makutu anu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 26

Onani Yeremiya 26:11 nkhani