Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 25:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

taonani, Ine ndidzatuma ndi kutenga mabanja onse a kumpoto, ati Yehova, ndipo ndidzatuma kwa Nebukadirezara mfumu ya ku Babulo, mtumiki wanga, ndipo ndidzatengera iwo pa dziko lino, ndi pa okhalamo ace onse, ndi pa mitundu iyi yozungulira, ndipo ndidzathetsa iwo ndithu, ndi kuwayesa iwo cizizwitso, ndi cotsonyetsa, ndi bwinja lamuyaya.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 25

Onani Yeremiya 25:9 nkhani