Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 25:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti, taonani, ndiyamba kucita coipa pa mudzi umene uchedwa ndi dzina langa, kodi inu mudzakhala osalangidwa konse? Simudzakhala osalangidwa; pakuti ndidzaitana lupanga ligwe pa onse okhala m'dziko lapansi, ati Yehova wa makamu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 25

Onani Yeremiya 25:29 nkhani