Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 25:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti mitundu yambiri ndi mafumu akuru adzayesa iwo atumiki ao; ndipo ndidzabwezera iwo monga mwa macitidwe ao, monga mwa nchito ya manja ao.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 25

Onani Yeremiya 25:14 nkhani