Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 25:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudzakhala, zitapita zaka makumi asanu ndi awiri, ndzidzalanga mfumu ya ku Babulo, ndi mtundu uja womwe, ati Yehova, cifukwa ca mphulupulu zao, ndi dziko la Akasidi; ndipo ndidzaliyesa mabwinja amuyaya.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 25

Onani Yeremiya 25:12 nkhani